Bible Lingo
Heaven Kumwamba
Earth
Dziko lapansi
Hell Gahena
Satan Satana
God
Mulungu
Spirit
Mzimu
Holy Spirit Mzimu woyera
Life
Moyo
Eternal Life
Moyo wosatha
Love
Chikonda
Joy
Chimwemwe
Peace
Mtendere
Heart
Mtima
Pastor
Mbusa
Ndikufuna kupita ku tchalitchi
Chipatso za mzimu ndipo chikonda, chimwemwe, mtendere, …
Ndinakonda anthu a ku Malawi ndi mtima wanga wonse.
Yesu anapatsa moyo wosatha.
Paciyambi Mulungu adalenga kumwamba ndi dziko lapansi
Yesu ananena naye, Ine ndine njira, ndi coonadi, ndi moyo. Palibe munthu adza kwa Atate, koma mwa Ine.